Joshua 2:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wina akadzatuluka m'nyumbamo kuti azidzayenda mu mseu, izo adzaone nzake, ife sitidzapalamula kanthu. Koma wina aliyense wokhala m'nyumba mwakomo akadzaona tsoka, mlandu udzakhala wathu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzakhala kuti aliyense akadzatuluka pa khomo la nyumba yako kubwalo, imfa imeneyi ndi yake, tilibe kupalamula ife; koma aliyense adzakhala ndi iwe m'nyumba, likamfikira dzanja, imfa imeneyi ndi yathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati wina aliyense adzatuluka mʼnyumbamo kuti azikayendayenda mu msewu, magazi ake adzakhala pamutu pake, ife sitidzapalamula kanthu. Koma wina aliyense wokhala mʼnyumba mwakomo akadzaphedwa, mlandu udzakhala wathu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzakhala kuti ali yense akadzaturuka pa khomo la nyumba yako kubwalo, imfa imeneyi ndi yace, tiribe kuparamula ife; koma ali yense adzakhala ndi iwe m'nyumba, likamfikira dzanja, imfa imeneyi ndi yathu.