Joshua 2:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komanso, ukangoulula zimene tikuchitazi, ife sitidzasunga lonjezo lathu tachitali.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ukawulula chodzera ifecho tidzamasukira lumbiro lako watilumbiritsali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komanso iwe ukangowulula zimene ife tikuchitazi ndiye kuti ife sitidzasunga zimene talonjezazi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ukaulula codzera ifeco tidzamasukira lumbiro lako watilumbiritsali.