Joshua 2:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo azondi aŵiri aja adatsika kumapiri kuja, ndipo ataoloka mtsinje uja, adakafika kwa Yoswa, namusimbira zimene adakumana nazo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo amuna awiriwo anabwerera, natsika m'phirimo naoloka, nafika kwa Yoswa mwana wa Nuni, namfotokozera zonse zidawagwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake azondi awiri aja anayamba ulendo wobwerera kwawo. Anatsika ku mapiri kuja, nawoloka mtsinje mpaka anakafika kwa Yoswa mwana wa Nuni. Ndipo anamuwuza zonse zimene zinawachitikira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo amuna awiriwo anabwerera, natsika m'phirimo naoloka, nafika kwa Yoswa mwana wa Nuni, namfotokozera zonse zidawagwera.