Joshua 2:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adauza Yoswayo kuti, “Ife tatsimikizadi kuti Chauta watipatsa dziko lonselo. Anthu onse kumeneko akuchita nafe mantha kwambiri.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa Yoswa, Zoonadi, Yehova wapereka dziko lonse m'manja mwathu; ndiponso nzika zonse zasungunuka pamaso pathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anati kwa Yoswa, “Ndithu, Yehova wapereka dziko lonse mʼmanja mwathu. Anthu onse kumeneko akuchita nafe mantha.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa Yoswa, Zoonadi, Yehova wapereka dziko lonse m'manja mwathu; ndiponso nzika zonse zasungunuka pamaso pathu.