Joshua 2:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo nkuti ataŵakweza pa denga azondiwo, nkuŵabisa pansi pa mapesi padengapo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma adawakweretsa patsindwi, nawabisa ndi mitengo yanthamza yoyanika patsindwi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma nʼkuti atawakweza pa denga azondiwo ndi kuwabisa pansi pa mapesi a thonje amene iye anawayika pa dengapo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma adawakweretsa patsindwi, nawabisa ndi mitengo yanthamza yoyanika patsindwi.