Joshua 2:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
naŵauza kuti, “Ndikudziŵa kuti Chauta wakupatsani dziko lonseli, ndipo tonsefe tikuchita mantha, mitima yathu ili thithithi!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nati kwa amunawo, Ndidziwa kuti Yehova wakupatsani dzikoli, ndi kuti kuopsa kwanu kwatigwera, ndi kuti okhala m'dziko onse asungunuka pamaso panu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo anawawuza kuti, “Ine ndikudziwa kuti Yehova wakupatsani dziko lino ndipo tili ndi mantha. Anthu onse a mʼdziko lino ali ndi mantha chifukwa cha inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nati kwa amunawo, Ndidziwa kuti Yehova wakupatsani dzikoli, ndi kuti kuopsa kwanu kwatigwera, ndi kuti okhala m'dziko onse asungunuka pamaso panu.