Joshua 20:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero cha kuzambwe kwa mtsinje wa Yordani adapatula Kedesi m'dera la Galilea, m'dziko lamapiri la Nafutali. M'dziko lamapiri la Efuremu adapatula Sekemu, ndipo m'dziko lamapiri la Yuda adapatula Kiriyati-Ariba (ndiye kuti Hebroni).
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapatula Kedesi m'Galileya ku mapiri a Nafutali, ndi Sekemu ku mapiri a Efuremu, ndi mudzi wa Ariba ndiwo Hebroni ku mapiri a Yuda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho iwo anapatula Kedesi mʼdera la Galileya ku mapiri a Nafutali, Sekemu ku mapiri a Efereimu, ndi Kiriati Ariba (ndiye Hebroni) ku mapiri a Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapatula Kedesi m'Galileya ku mapiri a Nafitali, ndi Sekemu ku mapiri a Efraimu, ndi mudzi wa Ariba ndiwo Hebroni ku mapiri a Yuda.