Joshua 21:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kwa zidzukulu za Aroni, ku banja lina limodzi la Akohati amene anali Alevi, maina ake ndi aŵa:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti ikhale ya ana a Aroni a mabanja a Akohati, a ana a Levi, pakuti maere oyamba adatulukira iwowa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ku banja la Kohati amene anali Alevi. Paja maere oyamba anagwera mabanja a Kohati kuti alandira mizinda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti ikhale ya ana a Aroni a mabanja a Akohati, a ana a Levi, pakuti maere oyamba adaturukira iwowa.