Joshua 21:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mabanja osiyanasiyana a Ageresoni adalandira mizinda khumi ndi itatu, kuphatikizapo mabusa a zoŵeta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Midzi yonse ya Ageresoni monga mwa mabanja ao ndiyo midzi khumi ndi itatu ndi mabusa ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mabanja onse a Ageresoni analandira mizinda 13 pamodzi ndi malo awo odyetsera a ziweto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Midzi yonse ya Agerisoni monga mwa mabanja ao ndiyo midzi khumi ndi itatu ndi mabusa ao.