Joshua 21:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mizinda 48 ya m'dziko limene Aisraele adalandira idapatsidwa kwa Alevi, pamodzi ndi mabusa a zoŵeta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Midzi yonse ya Alevi, pakati pa cholowa cha ana a Israele ndiyo midzi makumi anai kudza isanu ndi itatu, ndi mabusa ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Motero mizinda 48 ya mʼdziko limene Aisraeli analanda inapatsidwa kwa Alevi, kuphatikizapo malo ake odyetsera ziweto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Midzi yonse ya Alevi, pakati pa colowa ca ana a Israyeli ndiyo midzi makumi anai kudza isanu ndi itatu, ndi mabusa ao.