Joshua 21:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Akohati otsalawo adapatsidwa mizinda khumi kuchokera m'mafuko a Efuremu ndi Dani ndiponso theka la fuko la Manase lokhala kuzambwe kwa Yordani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana otsala a Kohati analandira molota maere motapa pa mabanja a fuko la Efuremu, ndi pa fuko la Dani, ndi pa fuko la Manase logawika pakati, midzi khumi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mabanja otsala a Kohati anapatsidwa mizinda khumi kuchokera ku mafuko a Efereimu, Dani ndi theka la fuko la Manase.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana otsala a Kohati analandira molota maere motapa pa mabanja a pfuko la Efraimu, ndi pa pfuko La Dani, ndi pa pfuko La Manase logawika pakati, midzi khumi.