Joshua 21:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraele onse pamodzi adapereka mizinda imeneyi kwa Alevi mwamaere, pamodzinso ndi mabusa odyetsapo zoŵeta, potsata zomwe Chauta adaalamula kudzera mwa Mose.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Motero ana a Israele anapatsa Alevi midzi iyi ndi mabusa ao, molota maere, monga Yehova adalamulira mwa dzanja la Mose.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Aisraeli anapereka kwa fuko la Levi mizindayi pamodzi ndi malo odyetserako ziweto pogwiritsa ntchito maere, monga Yehova analamula kudzera mwa Mose.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Motero ana a Israyeli anapatsa Alevi midzi iyi ndi mabusa ao, molota maere, monga Yehova adalamulira mwa dzanja la Mose.