Joshua 21:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mizinda ya Yuda ndi Simeoni imene idapatsidwa
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapatsa motapa pa fuko la ana a Yuda, ndi pa fuko la ana a Simeoni, midzi iyi yotchulidwa maina ao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awa ndi mayina a mizinda ya mafuko a Yuda ndi Simeoni imene inaperekedwa kwa zidzukulu za Aaroni,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapatsa motapa pa pfuko la ana a Yuda, ndi pa pfuko la ana a Simeoni, midzi iyi yochulidwa maina ao;