Joshua 22:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Aisraele atamva zimenezi, onse pamodzi adasonkhana ku Silo, kuti apite kukamenyana nawo nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene ana a Israele anamva ichi msonkhano wonse wa ana a Israele anasonkhana ku Silo, kuti awakwerere kuwathira nkhondo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
gulu lonse la Aisraeli linasonkhana ku Silo kuti lipite kukachita nawo nkhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene ana a Israyeli anamva ici msonkhano wonse wa ana a Israyeli anasonkhana ku Silo, kuti awakwerere kuwathira nkhondo.