Joshua 22:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo Aisraelewo adatuma Finehasi, mwana wa wansembe Eleazara kwa anthu a fuko la Rubeni ndi la Gadi ndiponso a theka lina lija la Manase, amene ankakhala ku dziko la Giliyadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Israele anatumiza kwa ana a Rubeni, ndi ana a Gadi, ndi fuko la Manase logawika pakati, ku dziko la Giliyadi, Finehasi mwana wa Eleazara wansembe,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Aisraeli anatumiza Finehasi mwana wa wansembe, Eliezara ku dziko la Giliyadi kwa mafuko a Rubeni, Gadi ndi theka la fuko la Manase.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Israyeli anatumiza kwa ana a Rubeni, ndi ana a Gadi, ndi pfuko la Manase logawika pakati, ku dziko la Gileadi, Pinehasi mwana wa Eleazare wansembe,