Joshua 22:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adafika ku dziko la Giliyadi, naŵauza anthu a fuko la Rubeni, la Gadi ndi theka lina lija la fuko la Manase kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'mene anafika kwa ana a Rubeni, ndi ana a Gadi, ndi fuko la Manase logawika pakati, ku dziko la Giliyadi, ananena nao ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atafika ku Giliyadi anawuza fuko la Rubeni, Gadi ndi theka lija la fuko la Manase kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mene anafika kwa ana a Rubeni, ndi ana a Gadi, ndi pfuko la Manase logawika pakati, ku dziko la Gileadi, ananena nao ndi kuti,