Joshua 22:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumbukirani tchimo la ku Peori lija limene Chauta adalanga nalo anthu ake poŵatumizira mliri woopsa. Mpaka lero lino, tchimo limene lija tidakasauka nalobe. Kodi tchimo limene lija ndi lochepa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi mphulupulu ya ku Peori itichipera, imene sitinadziyeretsera mpaka lero lino, ungakhale mliri unadzera msonkhano wa Yehova,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi tchimo lija la ku Peori ndi lochepa kwa inu? Paja Yehova analanga gulu lonse ndi mliri chifukwa cha tchimolo, ndipo mpaka lero tchimo limene lija tikanazunzika nalobe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi mphulupulu ya ku Peori iticepera, imene sitinadziyeretsera mpaka lero lino, ungakhale mliri unadzera msonkhano wa Yehova,