Joshua 22:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi tsopano mufuna kuleka kutsata Chauta, Mulungu wanu? Mukampandukira lero lino, Iye adzakwiyira mtundu wonse wa Aisraele maŵamaŵali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti mubwerera lero lino kusatsata Yehova? Ndipo kudzakhala kuti popeza lero mupikisana ndi Yehova, mawa adzakwiyira msonkhano wonse wa Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi inu tsono mufuna kupatuka kuleka kumutsata Yehova? “ ‘Ngati lero mumupandukira Yehovayo, ndiye kuti mawamawali Iye adzakwiyira gulu lonse wa Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti mubwerera lero line kusatsata Yehova? ndipo kudzakhala kuti popeza lero mupikisana ndi Yehova, mawa adzakwiyira msonkhano wonse wa Israyeli.