Joshua 22:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adaŵauza kuti, “Zonse zimene Mose mtumiki wa Chauta adakulamulani kuti muchite, mwachitadi, ndipo mwamvera malamulo anga onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nanena nao, Mwasunga inu zonsezo anakulamulirani Mose mtumiki wa Yehova; mwamveranso mau anga m'zonse ndinakulamulirani inu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo anawawuza kuti, “Inu mwachita zonse zimene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulani, ndipo mwamvera mu zonse zimene ndinakulamulirani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nanena nao, Mwasunga inu zonsezo anakulamulirani Mosemtumiki wa Yehova; mwamveranso mau anga m'zonse ndinakulamulirani inu;