Joshua 22:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumbukirani kuti Akani, mwana wa Zera uja, adakana kumvera lamulo la zinthu zoyenera kuwonongedwa zija, ndipo Aisraele onse adalangidwa. Akaniyo sadafe yekha chifukwa cha tchimo lakelo.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi Akani mwana wa Zera sanalakwe m'choperekedwacho, ndipo mkwiyo unagwera msonkhano wonse wa Israele? Osangoonongeka yekha munthuyo mu mphulupulu yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumbukirani pamene Akani mwana wa Zera anakana kumvera lamulo la zinthu zoyenera kuwonongedwa, kodi suja mkwiyo wa Yehova unagwera gulu lonse la Israeli? Akaniyo sanafe yekha chifukwa cha tchimo lakelo.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi Akani mwana wa Zera sanalakwa m'coperekedwaco, ndipo mkwiyo unagwera msonkhano wonse wa Israyeli? osangoonongeka yekha munthuyo mu mphulupulu yace.