Joshua 22:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraele anzanu simudaŵasiye nthaŵi yonseyi mpaka lero lino. Mwasamaladi malamulo onse a Chauta, Mulungu wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
simunasiya abale anu masiku awa ambiri mpaka lero lino, koma mwasunga chisungire lamulo la Yehova Mulungu wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aisraeli anzanu simunawasiye nthawi yayitali yonseyi mpaka lero lino. Inu mwaonetsetsa kuti mwachita zonse zimene Yehova anakulamulani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
simunasiya abale anu masiku awa ambiri mpaka lero lino, koma mwasunga cisungire lamulola Yehova Mulungu wanu.