Joshua 22:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mau adafotokozawo adakondwetsa Aisraele onse. Adatamanda Mulungu, ndipo sadakambenso za nkhondo yokaononga dziko limene anthu a mafuko a Rubeni ndi Gadi ankakhalamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mauwo anakomera ana a Israele pamaso pao; ndi ana a Israele analemekeza Mulungu, osanenanso za kuwakwerera ndi kuwathira nkhondo, kuliononga dziko lokhalamo ana a Rubeni ndi ana a Gadi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mawu amenewa anakondweretsa Aisraeli onse ndipo anayamika Mulungu. Choncho sanakambenso zopita ku nkhondo kukawononga dziko limene Arubeni ndi Agadi ankakhalamo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mauwo anakomera ana a Israyeli pamaso pao; ndi ana a Israyeli analemekeza Mulungu, osanenanso za kuwakwerera ndi kuwathira nkhondo, kuliononga dziko lokhalamo ana a Rubeni ndi ana a Gadi.