Joshua 22:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho anthu a mafuko a Rubeni ndi Gadi adalitcha guwalo kuti Mboni, chifukwa iwowo adati, “Chimenechi ndi mboni kwa tonsefe kuti Chauta ndi Mulungudi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Rubeni ndi ana a Gadi analitcha guwa la nsembelo: Ndilo mboni pakati pa ife kuti Yehova ndiye Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Arubeni ndi Agadi anatcha guwalo kuti Mboni: Mboni pakati pathu kuti Yehova ndi Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Rubeni ndi: ana a Gadi analicha guwa la nsembelo: Ndilo mboni pakati pa ife kuti Yehova ndiye Mulungu.