Joshua 22:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka Yoswa adaŵadalitsa anthuwo, naŵauza kuti apite. Tsono anthuwo adapita kwao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Momwemo Yoswa anawadalitsa, nawauza amuke; ndipo anamuka ku mahema ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yoswa anawadalitsa ndi kuwalola kuti apite ndipo anapitadi ku nyumba zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Momwemo Yoswa anawadalitsa, nawauza amuke; ndipo anamuka ku mahema ao.