Joshua 23:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukabwerera m'mbuyo ndi kuphatikizana ndi mitundu yotsalira ili pakati panuyi, ndi kumakwatirana nayo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma, mukadzabwerera m'mbuyo pang'ono pokha ndi kuumirira otsala a mitundu awa, ndiwo akutsala pakati pa inu, ndi kukwatitsana nao, ndi kulowana nao, naonso kulowana nanu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma ngati mubwerera mʼmbuyo ndi kuphatikizana ndi mitundu yotsalayi imene ili pakati panu ndi kumakwatirana nayo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma, mukadzabwereram'mbuyo pang'ono pokha ndi kuumirira otsala a mitundu awa, ndiwo akutsala pakati pa inu, ndi kukwatitsana nao, ndi kulowana nao, naonso kulowana nanu;