Joshua 23:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tamvani tsono, mitundu imene simudaipambanebe, ndaipereka kwa mafuko anu, chimodzimodzi mitundu inayo imene ndidaiwononga pakati pa Yordani ndi Nyanja Yaikulu kuzambweko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, ndakugawirani mitundu ya anthu iyi yotsala ikhale cholowa cha mafuko anu, kuyambira ku Yordani, ndi mitundu yonse ya anthu ndinaipasula, mpaka ku Nyanja Yaikulu ku malowero a dzuwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono onani! Mitundu ya anthu otsalawa ndayipereka kwa mafuko anu pamodzi ndi mitundu ya anthu ya pakati pa Yorodani ndi Nyanja Yayikulu ya kumadzulo imene ndinayigonjetsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, ndakugawirani mitundu ya anthu iyi yotsala ikhale colowa ca mapfuko anu, kuyambira ku Yordano, ndi mitundu yonse ya anthu ndinaipasula, mpaka ku nyanja yaikuru ku malowero a dzuwa.