Joshua 23:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero, muchenjere kuti mumvere ndi kumachitadi zonse zomwe zidalembedwa m'buku la malamulo a Mose. Musanyozere gawo lina lililonse la malamulowo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mulimbike mtima kwambiri kusunga ndi kuchita zonse zolembedwa m'buku la chilamulo cha Mose, osachipatukira kulamanja kapena kulamanzere;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Choncho khalani amphamvu, ndipo samalani kuti mumvere zonse zimene zalembedwa mʼbuku la malamulo a Mose. Musapatuke pa malamulo onse amene alembedwamo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mulimbike mtima kwambiri kusunga ndi kucita zonse zolembedwa m'buku la cilamulo ca Mose, osacipambukira kulamanja kapena kulamanzere;