Joshua 23:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo musagwirizane ndi anthu aŵa amene atsala pakati panu. Musamatchula maina a milungu yao kapena kulumbira poitchula, kapena kumaitumikira, kapenanso kumaigwadira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
osalowa pakati pa amitundu awa otsala mwa inu; kapena kutchula dzina la milungu yao; osalumbiritsa nalo, kapena kuitumikira, kapena kuigwadira;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musagwirizane ndi mitundu ya anthu imene yatsala pakati panu. Musatchule mayina a milungu yawo kapena kuyitchula polumbira. Musayitumikire kapena kuyigwadira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
osalowa pakati pa amitundu awa otsala mwa inu; kapena kuchula dzina la milungu yao; osalumbiritsa nalo, kapena kuitumikira, kapena kuigwadira;