Joshua 23:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adzakupirikitsirani mitundu yaikuluikulu ndi yamphamvu. Mpaka pano, palibe ndi mmodzi yemwe wotha kulimbana nanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova anaingitsa pamaso panu mitundu yaikulu ndi yamphamvu; koma inu, palibe munthu anaima pamaso panu mpaka lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yehova wapirikitsa patsogolo panu mitundu ya anthu ikuluikulu ndi yolimba. Mpaka lero palibe amene watha kulimbana nanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova anaingitsa pamaso panu mitundu yaikuru ndi yamphamvu; koma inu, palibe munthu anaima pamaso panu mpaka lero lino.