Joshua 24:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo anthuwo adayankha kuti, “Zoti nkusiya Chauta ndi kumakatumikira milungu ina ndiye ai, ife sitingathe kuchita zotere mpang'ono pomwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu anayankha, nati, Sikungatheke kuti timsiye Yehova, ndi kutumikira milungu ina;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anthu anayankha, “Sizingatheke kuti timusiye Yehova ndi kutumikira milungu ina!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu anayankha, nati, Sikungatheke kuti timsiye Yehova, ndi kutumikira milungu yina;