Joshua 24:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ife tikufika, Chauta ankapirikitsa Aamori amene ankakhala m'dziko lino. Motero nafenso tidzatumikira Chauta, chifukwa ndiye Mulungu wathu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo Yehova anaingitsa pamaso pathu anthu awa onse, ngakhale Aamori okhala m'dzikomo; chifukwa chake ifenso tidzatumikira Yehova, pakuti ndiye Mulungu wathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife tikufika Iye anapirikitsa anthu onse pamodzi ndi Aamori amene ankakhala mʼdzikoli. Ifenso tidzatumikira Yehova chifukwa Iye ndiye Mulungu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo Yehova anaingitsa pamaso pathu anthu awa onse, ngakhale Aamori okhala m'dzikomo; cifukwa cace ifenso tidzatumikira Yehova, pakuti ndiye Mulungu wathu.