Joshua 24:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Yoswa adauza anthuwo kuti, “Mwina mwaketu inu simungathe kutumikira Chauta chifukwa ndi Mulungu woyera, wosalola kupikisana naye. Ndipo sadzakulekererani mukumpandukira ndi kumamchimwira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa anati kwa anthu, Simukhoza inu kutumikira Yehova pakuti ndiye Mulungu woyera, ndi Mulungu wansanje; sadzalekerera zolakwa zanu, kapena zochimwa zanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yoswa anati kwa anthuwo, “Inutu simungathe kutumikira Yehova. Iye ndi Mulungu woyera, salola kupikisana naye. Sadzakukhululukirani ngati mumuwukira ndi kumuchimwira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa anati kwa anthu, Simukhoza inu kutumikira Yehova pakuti ndiye Mulungu woyera, ndi Mulungu wansanje; sadzalekerera zolakwa zanu, kapena zocimwa zanu.