Joshua 24:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo anthuwo adauza Yoswa, kuti, “Iyai! Ife tidzatumikira Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu anati kwa Yoswa, Iaitu, koma tidzatumikira Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthuwo anati kwa Yoswa, “Ayi! Ife tidzatumikira Yehova.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu anati kwa Yoswa, Iaitu, koma tidzatumikira Yehova.