Joshua 24:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yoswa adaŵauza kuti, “Inu mukudzichitira nokha umboni kuti mwasankhula kutumikira Chauta.” Anthuwo adavomera kuti, “Inde, mboni ndife tomwe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa ananena ndi anthu, Inu mwadzichitira mboni inu nokha kuti mwadzisankhira Yehova kumtumikira Iye. Ndipo anati, Ndife mboni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yoswa anati, “Inu mukudzichitira nokha umboni kuti mwasankha kutumikira Yehova.” Iwo anayankha kuti, “Inde ife ndife mboni.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa ananena ndi anthu, Inu mwadzicitira mboni inu nokha kuti mwadzisankhira Yehova kumtumikira iye. Ndipo anati, Ndife mboni.