Joshua 24:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yoswayo adalemba malamulo ameneŵa m'buku la malamulo a Mulungu, ndipo adatenga chimwala chachikulu nachiimiritsa patsinde pa mtengo wa thundu pa malo opatulika a Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa analembera mau awa m'buku la chilamulo cha Mulungu; natenga mwala waukulu, nauimitsa apo patsinde pa thundu wokhala pa malo opatulika a Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yoswa analemba zinthu izi mʼbuku la malamulo a Mulungu. Kenaka iye anatenga mwala waukulu nawuyimika pansi pa mtengo wa thundu pa malo wopatulika a Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa analembera mau awa m'buku la cilamulo ca Mulungu; natenga mwala waukuru, nauimitsa apo patsinde pa thundu wokhala pa malo opatulika a Yehova.