Joshua 24:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adauza anthuwo kuti, “Mwala umenewu udzakhala mboni yotitsutsa. Mau amene Chauta walankhula ndi ifeŵa, mwalawu wamva. Motero udzakhala mboni yokutsutsani, ngati mudzakane Mulungu wanu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa anati kwa anthu onse, Taonani, mwala uwu udzakhala mboni yotitsutsa; pakuti udamva mau onse a Yehova amene ananena kwa ife; ndipo udzakhala mboni yotsutsa inu, mungakanize Mulungu wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yoswa anati kwa anthu onse, “Tamvani! Mwala uwu udzakhala mboni yotitsutsa. Mwalawu wamva mawu onse amene Yehova wayankhula kwa ife. Udzakhala mboni yotitsutsa ngati mukhala osakhulupirika kwa Mulungu wanu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa anati kwa anthu onse, Taonani, mwala uwu udzakhala mboni yotitsutsa; pakuti udamva mau onse a Yehova amene ananena kwa ife; ndipo udzakhala mboni yotsutsa inu, mungakanize Mulungu wanu.