Joshua 24:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yoswa adaŵalola anthuwo kuti aliyense abwerere ku dziko lake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Yoswa anauza anthu amuke, yense ku cholowa chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yoswa analola anthu kuti apite, aliyense ku dera lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Yoswa anauza anthu amuke, yense ku colowa cace.