Joshua 24:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zitatha zimenezi, Yoswa mwana wa Nuni, mtumiki wa Chauta, adamwalira. Anali ndi zaka 110 zakubadwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, zitatha izi, Yoswa mwana wa Nuni mtumiki wa Yehova, adafa, wa zaka zana ndi khumi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zitatha zinthu izi, Yoswa mwana wa Nuni, mtumiki wa Yehova, anamwalira ali ndi zaka 110,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, zitatha izi, Yoswa mwana wa Nuni mtumiki wa Yehova, adafa, wa zaka zana ndi khumi.