Joshua 24:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Eleazara, mwana wa Aroni, nayenso adamwalira, ndipo adamuika ku Gibea m'mudzi wa mwana wake Finehasi, umene adaamupatsa m'dziko lamapiri la Efuremu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Eleazaranso mwana wa Aroni anafa; ndipo anamuika pa phiri la Finehasi mwana wake, limene adampatsa ku mapiri a Efuremu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Eliezara mwana wa Aaroni anamwalira ndipo anayikidwa mʼmanda ku Gibeya, malo amene anapatsidwa kwa Finehasi mwana wake, mʼdziko lamapiri la Efereimu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Eleazarenso mwana wa Aroni anafa; ndipo anamuika pa phiri la Pinehasi mwana wace, limene adampatsa ku mapiri a Efraimu.