Joshua 24:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nditatulutsa makolo anu ku dziko la Ejipito, ndidafika nawo ku Nyanja Yofiira, koma Aejipito okwera pa magaleta ndi pa akavalo adaŵatsatira mpaka kunyanjako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinatulutsa atate anu m'Ejipito; ndipo munadza kunyanja; koma Aejipito analondola atate anu ndi magaleta ndi apakavalo mpaka ku Nyanja Yofiira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nditatulutsa makolo anu ku Igupto ndinafika nawo ku Nyanja Yofiira. Aigupto anawathamangira ndi magaleta ndi okwera pa akavalo mpaka ku Nyanja Yofiira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinaturutsa atate anu m'Aigupto; ndipo munadzakunyanja; koma Aaigupto analondola atate anu ndi magareta ndi apakavalo mpaka ku Nyanja Yofiira.