Joshua 3:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Yoswa adauza anthu onse kuti, “Mudzisungetu tsono, chifukwa maŵa Chauta adzachita zodabwitsa zazikulu pakati panu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa ananena kwa anthu, Mudzipatule, pakuti mawa Yehova adzachita zodabwitsa pakati pa inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yoswa anawuza anthu kuti, “Dzipatuleni tsono pakuti mawa Yehova adzachita zodabwitsa pakati panu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa ananena kwa anthu, Mudzipatule, pakuti mawa Yehova adzacita zodabwiza pakati pa inu.