Joshua 3:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maŵa mwake Yoswa adauza ansembe kuti, “Nyamulani Bokosi lachipangano la Chauta, muwoloke, mutsogolere anthuwo.” Iwowo adachitadi monga momwe Yoswa adanenera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa anati kwa ansembe, Senzani likasa la chipangano, nimuoloke pamaso pa anthu. Nasenza iwo likasa la chipangano, natsogolera anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmawa mwake Yoswa ananena kwa ansembe kuti, “Nyamulani Bokosi la Chipangano muwoloke ndipo mukhale patsogolo pa anthu.” Motero iwo analinyamula ndi kupita patsogolo pawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa anati kwa ansembe, Senzani likasa la cipangano, nimuoloke pamaso pa anthu. Nasenza iwo likasa la cipangano, natsogolera anthu.