Joshua 4:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtundu wonse wa Aisraele utaoloka Yordani, Chauta adauza Yoswa kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, utatha kuoloka Yordani mtundu wonse, Yehova ananena ndi Yoswa, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse atatha kuwoloka Yorodani, Yehova anati kwa Yoswa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, utatha kuoloka Yordano mtundu wonse, Yehova ananena ndi Yoswa, nati,