Joshua 4:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yoswa adaŵalamuladi kuti atuluke.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Yoswa analamulira ansembe, ndi kuti, Kwerani kutuluka m'Yordani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Yoswa anawalamuladi ansembe aja kuti atuluke mu Yorodani muja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Yoswa analamulira ansembe, ndi kuti, Kwerani kuturuka m'Yordano.