Joshua 4:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Sankha amuna khumi ndi aŵiri, mmodzi pa fuko lililonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzitengere mwa anthu, amuna khumi ndi awiri, fuko limodzi mwamuna mmodzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Sankha amuna khumi ndi awiri, mmodzi pa fuko lililonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzitengere mwa anthu, amuna khumi ndi awiri, pfuko limodzi mwamuna mmodzi;