Joshua 4:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumeneko ndiko kumene Yoswa adaimiritsa miyala khumi ndi iŵiri ija imene adaaitenga ku Yordani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa anaimika ku Giligala miyala ija khumi ndi iwiri adaitenga m'Yordani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ku Giligala, Yoswa anayimikako miyala khumi ndi iwiri imene anayitenga mu Yorodani ija.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa anaimika ku Giligala miyala ija khumi ndi iwiri adaitenga m'Yordano.