Joshua 4:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adauza Aisraele onse aja kuti, “Ana akamadzafunsa makolo ao m'tsogolo muno kuti, ‘Kodi miyala imeneyi imatanthauzanji?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa ana a Israele, Ana anu akadzafunsa atate ao masiku akudza, ndi kuti, Miyala iyi nja chiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo iye anati kwa Aisraeli, “Mʼtsogolo muno pamene adzukulu anu adzafunsa makolo awo kuti, ‘Kodi miyala iyi ikutanthauza chiyani?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa ana a Israyeli, Ana anu akadzafunsa atate ao masiku akudza, ndi kuti, Miyala iyi nja ciani?