Joshua 4:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha chimenechi, aliyense pa dziko lapansi pano adzadziŵa mphamvu za Chauta, ndipo mudzalemekeza Chauta, Mulungu wanu, mpaka muyaya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti mitundu yonse ya pa dziko lapansi idziwe dzanja la Yehova, kuti ndilo lamphamvu; kuti iope Yehova Mulungu wanu masiku onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anachita zimenezi kuti anthu onse pa dziko lapansi adziwe kuti dzanja la Yehova ndi lamphamvu, ndi kuti inu muziopa Yehova Mulungu wanu masiku onse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti mitundu yonse ya pa dziko lapansi idziwe dzanja la Yehova, kuti ndilo lamphamvu; kuti lope Yehova Mulungu wanu masiku onse.