Joshua 4:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono uŵalamule kuti, ‘Tengani miyala khumi ndi iŵiri pakati penipeni pa mtsinje wa Yordanipo, pa malo amene anali kuimirira ansembewo. Nyamulani miyala imeneyo ndi kudza nayo ku zithando zanu kumene mudzagone usiku.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo muwalamulire iwo ndi kuti, Mudzitengere pano pakati pa Yordani, poimapo mapazi a ansembe, miyala khumi ndi iwiri, ndi kuoloka nayo, ndi kuiika m'mogona m'mene mugonamo usiku uno.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono uwalamule kuti, ‘Tengani miyala khumi ndi iwiri pakati penipeni pa mtsinje wa Yorodani, pamalo pamene ansembe anayimirirapo. Miyalayo muwoloke nayo ndi kudzayitula pamalo pamene mukagone usiku uno.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo muwalamulire iwo ndi kuti, Mudzitengere pano pakati pa Yordano, poimapo mapazi a ansembe, miyala khumi ndi iwiri, ndi kuoloka nayo, ndi kulika m'mogona m'mene mugonamo usiku uno.