Joshua 4:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo adaŵalamula kuti, “Loŵani mu mtsinje wa Yordaniwu patsogolo pa Bokosi lachipangano la Chauta, Mulungu wanu. Aliyense mwa inu atenge mwala pa phewa. Fuko lililonse la Aisraele litenge mwala umodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nanena nao Yoswa, Olokani, kutsogolera likasa la Yehova Mulungu wanu pakati pa Yordani, nimudzisenzere yense mwala paphewa pake, monga mwa kuwerenga kwa mafuko a ana a Israele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo anawawuza kuti, “Lowani pakati pa mtsinje wa Yorodani, patsogolo pa Bokosi la Yehova Mulungu wanu. Ndipo aliyense wa inu atenge mwala pa phewa lake, monga mwa chiwerengero cha mafuko a Aisraeli,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nanena nao Yoswa, Olokani, kutsogolera likasa la Yehova Mulungu wanu pakati pa Yordano, nimudzisenzere yense mwala paphewa pace, monga mwa kuwerenga kwa mapfuko a ana a Israyeli;